Agalatiya4

1Chipano nikamba chimwechi olanja wakakhala wakali mwana, siwasiyana ni kapolo, hata ngati chuma chonjhe ni chake.2Ndhawi imeneyo wakhala panjhi pa wandhu amlela ni akumsunga mbaka yapo siijhe ndhawi ijha idaikidwa ni atate wake.3Chimwecho ni ife yapo tidali tikali wana, nafenjho chichijha tidali ngati wana tidalamuludwa vindhu va jhiko lino.4Nambho ndhawi yeneyene yapo idakwana Amnungu adamtuma Mwana wao uyo pajhiko lino la panjhi. Mwana uyo wadabadwa ni wamkazi, mwana mmeneyo wadachgozedwa ni thauko la Musa,5waombole anyiwajha achogozedwa ni thauko, dala ife Ayahudi tichitidwe kukhala wana Amnungu.
6Ndande chipano anyiimwe ni wanawake, Amnungu wautuma mzimu wa mwanawake mmitima mwanu, mzimu uwo utichita kuti timtane Mnungu, “Atate wathu.”7Chimwecho anyiimwe asati akapolonjho nambho niwana, ni ikakhala anyiimwe nimwana, basi simulandile yonjhe yayo Mnungu waikila wana wake.
8Kale yapo simmamjhiwe Mnungu, chimwecho mmatumikila minungu iyo idali asati Mnungu wa zene.9Nambho saino pakuti mwamjhiwa Mnungu, kapina tikambe Mnungu wakujhiwani, mkhoza bwanji kubwela kutumikila thauko ni chikalidwe cha jhiko lino ni kufuna kuvitumilanjho?10Mkali kuchita pwando la siku, mwezi, nyengo ni vyaka.11Nikhaikila kuti ikhozekena njhito ijha nidaichita kwa anyiimwe, ikhozeka kuti yandotaika chajhe!
12Achabale nikupembhani mkhale ngati ine, simudachogozedwa ni thauko ngati ine umo nili. Yapo nidali kwanu simdanichitile choipa chilichonjhe.13Anyiimwe mjhiwa kuti utenda wanga ndeuwo udanichita nilalikile Uthenga wa Bwino kwa mala yoyamba.14Ata chimwecho ndhawi ijha simdaninyoze kapina kunikana ndande ya utenda wanga, ata ngati wina adakukambilani mchite chimwecho, nambho mdanilandila ngati mtumiki wa kumwamba wa Amnungu, ngati Kilisito Yesu mwene.15Myambo mdali wandhu okondwela, ndande chipano simkondwela? Nilumbila kuti ndhawi ijha mdakakoza ata kuyazula maso yanu ni kunipacha ine.16Bwanji, saino nakhala mdani wanu ndande ya kukukambilani uzene?17Achameneo wandu wina ajhichaucha ndande yanu, nambho sakuganizilani bwino. Afuna kukupatulani ni ine kuti anyiimwe mchauchichike ndande yao.18Uzene ni chindhu chabwino kupunda kwachitila wandhu wina vindhu vabwino, mchite chimwecho masiku yonjhe ata ngati nili Patali namwe.19Wana wanga, ngati mujha wavutikila maye uyo wali ni pathupi ndhawi yojhimasula, niine nivutika ndande yanu mbaka ukhalo yapo siuoneke mkati Kilisito.20Ngati nidakakala ni anyiimwe saino, nidakakamba kwa upole pakati panu! Pakuti nikhaikila kupunda ndande ya anyiimwe!
21Nikambileni, anyiimwe mkonda kulamulidwa ni thauko, bwanji mwavela umo likambila thauko?22Yalembedwa mmalembo ya Mnungu kuti Abilahimu wadali ni wana awili, mmojhi wadabala ni wamkazi uyo wadali kapolo ni mwina wadabala kwa mkazake mfulu.23Yujha wadabala ni kapolo wadabadwa ngati umo abadwila wina, nambho yujha wadabala ni mkazake mfulu wadabadwa kuchokana ni mujha wadakambila Mnungu.24Vindhu vimenevo vidali chifani, anyamaye awili ameneo ni chifani cha mapangano yawili, loyambila nilijha lidachitika kuphili ilo litanidwa sinai, ilo Ajhili ni wanawake wadabalila ku ukapolo.25Ajhili wali ngati phili la sinai ilo lili kwa Waalabu, ni chifani cha Mujhi wa Yelusalemu cha chipano, uwo uli kuukapolo pamojhi ni wana wake.26Nambho Yelusalemu ya kumwamba ni mujhi uwo siuli kuukapolo, nawo ni chifani cha maye wathu.27Pakuti yalembedwa, “Kondwela iwe wamkazi siubala, kweza mvekelo iwe siudajhimasulepo mwana, pakuti wana a yujha wasiidwa niambili, kupitilila wa yujha wali ni wammuna.”
28Chipano achabale wanga, anyiimwe ni wana a Mnungu kuchokana ni mujha wadakambila, ngati umo idali kwa Isaka.29Nambho ngati mujha siku zijha yujha mwana wadabadwila kwa njila iyo yazoeleledwa, wadamvutichya yujha mwana wadabadwa kwa mbhavu za Mzimu wa Mnungu, chimwecho nde umo ichitikila mbaka chipano.30Nambho malembo ya Mnungu yakamba bwanji? Yakamba chimwechi, “Mtopole wamkazi kapolo pamojhi ni mwana wake, pakuti mwana wa wamkazi kapolo siwalanjilatu pamojhi ni mwana wa wamkazi uyo osati kapolo.”31Chimwecho achabale wanga, ife asati wana a wamkazi kapolo, ife ni wana wa wamkazi uyo asati kapolo.

The Word for the World International

https://app.library.bible/content/5f84a5b042979396