1 Akolinso15
1Chipano nifuna kukumbuchani anyiimwe abale wanga, ujha Uthenga Wabwino nidakulalikilani, namwenjho mudaikhulupilila, ni kuima nganganga.2Kupitila Uthenga Wabwino mulamichidwa, ikakhala ngati mupotela njhito Uthenga uwo nidakulalikilani, ila ngati simusiye, kukhulupilila kwanu kudali kwachajhe.3Ine nidakupachani vindhu ivo nidavilandila, kuti Kilisito wadamwalila kwa ndande ya machimo yathu, ngati umo yalembedwela malembo ya Mnungu,4kuti wadazikidwa ni siku la katatu wadahyuka, ngati umoyalembedwela malembo ya Mnungu,5kuti wadamtulukila Kefa, ndiipo pambuyo wadaatulukila wajha khumi ni awili.6Pambuyo wadatulukila yawo amkhulipila Kilisito miathano, kwapamojhi, ambili wao akali amoyo, nambho wina adathomwalila.7Pambuyo wadamtulukila Yakobo, ndiipo wadatulukila atumwi wonjhe.8Pothela wadanitulukila ine Poolo uyo nidali ngati uyo wabadwa kwa njila yozizwicha.9Mateyake ine sinijhika ngati umo ajhiwikila atumwi wina, ni sinifunika kutanidwa mtumwi, ndande nidalivuticha gulu la wandhu amkhulupilila Yesu.10Nambho kwa ubwino wa Mnungu nali ngati umu nali, ni ubwino wake siudali chajhe, ine nachita njhito kupitilila atumwi wonjhe, osati ine nambho ubwino wa a Mnungu uchita njhito pamojhi ni ine.11Chimwecho, ikhale ine nidalalikila kapina anyiiwo atumwi wina adalakila Uthenga Wabwino, ata chimwecho taonjhe tilalikila Uthenga uwu uwo tidaukhulupilila.12Chipano, pakuti talalikila kuti Kilisito wadahyuka, mbona akumojhi wanu akamba wandhu akufa sahyuka?13Ngati palibe kuhyuka, basi ata Kilisito nayo siwadahyuke,14Ni ikakhala Kilisito siwadahyuke, basi kulalikila kwathu kulibe mate ni kukhulupilila kwanu kulibe mate.15Kupitilila yameneyo, ife tidakakhala amboni amthila pachogolo pa Mnungu, ndande tidakamba kuti Mnungu wadamhyukicha Kilisito, kumbe iye siwadamhyukiche, nambho limenelo silikhoza kukhala lazene kuti akufa siahyukichidwa.16Ikakhala zene wandhu akufa siahyukichidwa, ndekuti Kilisito nayo siwadahyukichidwe.17Ni ngati Kilisito siwada hyukichidwe, chikhulupi chanu nichachajhe, ni mkali mumachimo yanu.18Chimwecho ni onjhe anyiyao amwalila uku amkhulupila Kilisito atayika.19Ngati yajha tifuna kupata kuchoka kwa Kilisito ndande ya umoyo wathu wasazinope, ife ni wandhu tifunika kulengeledwa lisungu kupitilila wandhu onjhe pajhiko.20Nambho uzene Kilisito nde oyamba kuhyukichidwa ni Mnungu, kwa awajha amwalila ngati vipacho voyamba va mlimi.21Pakuti ngati mujha nyifa yapelekedwa pajhiko kupitila kwa mundhu mmojhi nde Adamu, chimwecho kuhyuka nako kwajha kupitila mundhu mmojhi nde Kilisito.22Ngati mujha kwa kulunjana ni Adamu wandhu wonjhe amwalila, chinchijha wonjhe sahyukichidwe kwa kulunjana ni Kilisito.23Nambho kila mmojhi siwahyuke kwa ndhawi yake, Kilisito wadali oyamba, nde sachatile anyiwajha ali wake ndhawi iyo siwajhe.24Pambuyo pa yameneyo, mathelo nde siyafike Kilisito yapo siwapache Amnungu Atate ufumu, pambuyo pa kutayila kutali kila mafumu, ulalilo ni mbhavu25Kilisito, wafunika walamulile, mbaka yapo Mnungu siwaike adani wake wonjhe panjhi pa ulamulilo wake.26Nyifa nde mdani wothela uyo siwayomwechedwe.27Malembo ya Mnungu yakamba, “Mnungu waika vindhu vonjhe panjhi pa ulamulilo wake.” Nambho malembo yapo yakamba, “Vindhu vonjhe vaikidwa panjhi pa ulamulilo wake dala wavilamule” Ili ni mate Mnungu siwalowa gulu limenelo la vindhu, mate iye nde waviika vindhu vimenevo panjhi pa Kilisito.28Nambho vindhu vonjhe vikatho ikidwa panjhi pa ulamulilo wa Kilisito, nde yapo iye nayo Mwana siwajhiike panjhi pa ulamulilo wa Mnungu, uyo waika vonjhe panjhi pa ulamulilo wake, dala Mnungu walamulile vonjhe.29Ngati palibe kuhyuka, bwanji wandhu anyiyao abatizidwa ndande ya anyiyao amwalila, apenyelela kupata chiyani? Ngati yao amwalila siahyukichidwa, kubatizidwa ndande yao kuli ni mate yanji?30Niife ndande yanji tali muhatali ndhawi zonjhe?31Achabale, ine niichata nyifa siku zonjhe! Kwa ufulu nilinawo kwaanyiimwe pakulunjana ni Kililsito Yesu Mbuye wathu inichita niuzile chindhu ichi.32Ngati, dala langa lidakali la chimundhupe, kujha kubulana kwanga ni wandhu yao adali ngati zinyama zokalipa pano pa Efeso kudakanithangatila chiyani? Ngati yao amwalila siahyuka basi, “Tidye ni kumwa ndande mawa sitimwalile.”33Msadanyengeka, “Mabwenji woyipa uwananga ukhalo wako.”34Ukani yambani kukhala bwino, nisiyani kuchita machimo. Akumojhi wanu siamujhiwilatu Mnungu, ichi nikukambilani ninjhoni yaikulu kwanu.35Nambho mundhu wakhoza kufunjha, “Yao amwalila siahyukichidwe bwanji? Siakhale ni thupi la bwanji?”36Anyiimwe asabwabwa! Ukavyala mbeu, ngati siifa ndekuti siimela.37Yapo muvyala, muvyala mbeupe, ikhozeka ya ngano mbeu kapina ina, ni osati mmela wambhumbhu uwo uchokela pambuyo38Nambho Mnungu wazipacha mbeu thupi, ngati mujha wafunila iye, kila mbeu zipheza thupi la lokha.39Mathupi ya voumbidwa vonjhe siyalingana, nambho matupi ya wandhu yamtundu umojhi, ni matupi ya zinyama niyamtundu umojhi, ni matupi ya mbalame niyamtundu umojhi, ni matupi ya njhomba niyamtundu umojhi.40Yalipo mathupi ya kumwamba ni yapajhiko, kukhadwa kwa matupi ya kumwamba nikwina, ni kukhadwa kwa matupi ya pajhiko nikwina.41Kukhadwa kwa jhua, kulekana ni kukhadwa kwa mwezi, ni kukhadwa kwa mwezi ulekana ni ndhondwa ata ndhondwa zene zileka kwa kukhadwa.42Chimwecho ndeumo siikhalile ndhawi ya kuhyukichidwa. Ngati ijha mbeu, thupi likwililidwa mndhaka ni liwanangika nambho lihyukichidwa lili lokhadwa.43Thupi lizikidwa lilibe mbhavu ni silikhadwa, nambho lihyukichidwa lililokhadwa, lijha thupi la vyalidwa popande mbhavu, lihyukichidwa kwa mbhavu.44Thupi yapo lizikidwa, likhala thupi la kawaida, yapo lihyukichidwa ni thupi la chizimu, ni kuli thupi lakawaida, ni thupi la chizimu.45Malembo yalembedwa, “Mundhu woyamba Adamu wadali choumbidwa chamoyo” Nambho Adamu wothela iye ni Mzimu uyo wapacha wandhu umoyo.46Nambho lichogolela kukhalako, opande thupi lijha la chizimu ila thupi la kawaida, ndiipo likujha thupi lijha la chizimu.47Mundhu woyamba yaani Adamu, wadaumbidwa kwa dothi, wadachoka mndhaka, mundhu wakawili yaani Kilisito wadachoka kumwamba.48Wonjhe ali ajhiko la panjhi ali ngati mundhu uyo wadaumbidwa kwa dothi, anyiwajha ali akumwamba ali ngati yujha wadachoka kumwamba.49Ngati mujha talingana ni yujha wadaumbidwa kwa dothi, chimwecho ndeumo sitilingane ni yujha wachoka kumwamba.50Achabale nikamba chimwechi, chijha chachitidwa kwa thupi ni mwazi sichikhoza kulunjana ni Ufumu wa Mnungu, niicho chiwanangika sichikhoza kukhala chosawanangike.51Vechelani nikukambilani chisisi ichi, ife sitimwalila taonjhe nambho taonjhe siting'anamulidwe,52Mwachizulumukila, ndhawi ya mbetete yothela yapo siilile, yao amwalila siahyukichidwe, nafe siting'anamulidwe ni kukhala ni matupi yayo siyakufanjho.53Mate thupi lowanangika, ifunika livale kosawanangika, ni dala thupi la kumwalila ifunika livale osamwalila.54Chimwecho thupi ili lakuwanangika yapo silivale kosawanangika, nalo thupi la kumwalila yapo sili vale kosamwalila, ndeyapo lijha mawu lalembedwa silikwanile “Nyifa yawanangidwa kwa kuikhoza!”55“Kuli pati kukhoza kwa nyifa? Kuli pati kuwawa kwa nyifa?”56Nyifa, ipata mbhavu ya kupweteka kuchoka kumachimo, ni machimo yapata mbhavu ya kupweteka kuchoka mthauko.57Nambho wayamikidwe Mnungu, iye watipacha kukhoza kwa kupitila Yesu Kilisito!58Chimwecho achabale wanga, imani nganganga msada tingizika. Mpunde kuichita njhito ya Ambuye, mate mjhiwa njhito ya Ambuye siitaika chajhe.
The Word for the World International