1 Akolinso13

1Ata ngati, nikamba kwa mikambo ya wandhu ni atumiki akumwamba a Mnungu, nambho ngati nilibe chikondi, nikhala ngati mvekelo wa chibekete ichochilibe kandhu kapina chingwangwa.2Ndiponjho ata ngati, nali ni mbhaso yolalikila Uthenga wa Mnungu, ni kujhiwa nghani zonjhe za Mnungu ni hekima zonjhe, atangati nali nichikhulupi chokwana mbaka kukhoza kuzula phili ngati nilibe chikondi ine asati kandhu.3Nikachocha kila chindhu, nikwapacha ausiwa, nikuchocha thupi langa libuchidwe nambho ngati nilibe chikondi, siinithangatila kandhu.
4Uyo wali ni chikondi waembekeza, wathangatila, uyo wali nichikondi walibe njhanje, walibe dama, kapina kujhiona,5uyo wali ni chikondi siwachepa ulemu, uyo wali ni chikondi siwafuna vindhu va kumthangatila mwene, kapina mbhwai za msanga, siwasunga chikumbukilo cha voipa,6mundhu wa chikondi siwakondwela voipa, nambho chikondwela uzene.7Mundhu wachikondi wapilila yonjhe, mundhu wa chikondi wakhulupila wina, mundhu wa chikondi waembekeza, ni siwalepela.
8Chikondi chiendekela sikuzonjhe, nambho ukakhalapo ulosi siuthele, ikakhalapo mikambo siithela kukakhalapo kujhiwa nako sikuthele.9Pakuti sitijhiwa kila kandhu, ni sitijhiwa kulalikila Uthenga wa Mnungu bwinobwino,10nambho pasiku zikujha sitijhiwe kila chindhu ngati umo chili, ni vijha tivijhiwa pang'ono sivisowe.
11Yapo nidali mwana wakhanda, mawu yanga, kujhiwa ni maganizo yanga yadali ngati mwana wakhanda, nambho chipano nakula vindhu vijha va ubwana navisiya.12Icho tichiona saino, chili ngati sitijhiona bwino pa chiyoo icho chili ni majhi, nambho pambuyo sitione kila chindhu padanga. Chipano tijhiwa pang'ono nambho pambuyo sitijhiwe uzene onjhe, ngati umo Mnungu watijhiwila ife bwino.
13Chipano sivikhalile vindhu ivi vitatu, kumkhulupilila Mnungu, kulandila vindhu kuchoka kwa Mnungu, ni kwakonda wina, nambho chindhu cha chikulu ni kwakonda wina.

The Word for the World International

https://app.library.bible/content/5f84a5b042979396