1 Akolinso11

1Nichatizeni ine ngati umo ine nimchatiza Kilisito.
2Nikuyelekelani ndande mwanikumbukila mu vindhu vonjhe ni kuyachata mayaluzo nidakupachani.3Nambho nifuna mjhiwe kuti Kilisito wali ni ulamuli kwa kila wammuna, ni wammuna wali niulamuli kwa mkazake, ni Mnungu wali ni ulamuli kwa Kilisito.4Chimwecho wammuna yapo wapembhela, kapina kuchocha ulosi uku wavinikila mutu mmeneyo siwamlemekeza Kilisito.5Ni wamkazi waliyonjhe yapo wapembhela, kapina kulalikila Uthenga Wabwino, popande kumanga njhalu kumutu wake mmeneyo siwamlemekeza mmunake, uyo wachita chimwecho walingana ni wamkazi uyo wameta mpala.6Ngati wamkazi siwadamange njhalu kumutu, basi wasenge machichi. Ningati ninjhoni wamkazi kupupa, kapina kumeta mpala, basi mbasa wamange njhalu kumutu.7Nambho wammuna siwadavinikila mutu, ndande iye ni chifani ni ulemelelo wa Mnungu. Nambho wamkazi ni chifani cha wammuna,8ndande imeneyo, wammuna siwadaumbidwe kuchokela kwa wamkazi, nambho wamkazi waumbidwa kuchokela kwa wammuna.9Wammuna siwadaumbidwe kuthangatila wamkazi, nambho wamkazi ndeuyo wadaumbidwa kumthangatila wammuna.10Chimwecho nde ndande wamkazi wamanga njhalu mutu wake, ikhale chizindikilo pamwamba pa ulamuli uli pamwamba pake, ndande ya kwa akondwecha atumiki akumwamba Amnungu.11Atamchimwecho, pachogolo pa Ambuye, wamkazi wamkhulupilila wammuna, nayo wammuna wamkhulupilila wamkazi.12Ngati mujha wamkazi waumbidwa kwa wammuna, nambho wammuna wabalidwa ni wamkazi, Mnungu nde uyo wachita vonjhe.
13Lamulani mwachinawene, ngati nibwino wamkazi wampembhe Mnungu popande kumanga njhalu kumutu.14Ata maumbidwe yene yatiyaluza kuti wammuna kukhala ni machichi ya mbili ninjhoni.15Nambho wamkazi wakakhala ni machichi yambili ni ufulu kwaiye. Nde ndande wapachidwa machichi yayatali dala yamvinikile.16Ngati mundhu wafuna kulimbana pa mwamba pa chindhu ichi, ndiipo wajhiwe kuti ife wala gulu la wandhu a Mnungu sitiijhiwa kuti umeneo nde mthethe wathu.
17Yapo niendekela kukuninghani maagizo yaya sinikhoza kukuyelekelani panghani yaya yachatila, Yapo mphezana kumlambila Mnungu anyiimwe mwakhulupilila zenedi vindhu voipa nde vichokela kupitilila vindhu vabwino.18Choyamba, navela yapomkomana pamojhi ngati gulu la wandhu amkhulupilila Yesu nivela mupatulana, nane nikhulupila pang'ono.19Mate yake ifunika pakhale nikupatulana pakati panu, dala kulangiza kuti achiyani yawo akhulupilila Yesu azene.20Zene yapo mkomana pamojhi, nambho simukudya chakudya cha Ambuye.21Pakuti kila mmojhi wakudya chakudya chake popande kudya ni mnjake, mbaka akumojhi wanu akhala ni njala, kapina akhala bila chakumwa, nambho wina akudya ni kumwa mbaka kulojhela.22Bwanji simkhoza kudya ni kumwa kumakomo yanu? Kapina mudelela gulu la wandhu amkhulupilila Kilisito, ni kwalengecha njhoni anyiyao alibe kandhu? Nikukambileni chiyani? Nikuyelekeleni? Notho osati kwa yameneyo!
23Pakuti ine nidalandila kwa Ambuye yajha mayaluzo nidakupelekelani, kuti usiku ujha Ambuye Yesu, yapo wadachochedwa wadatenga bumunda,24wadamuyamika Mnungu, wadaubandhula, wadakamba, “Ili nithupi langa, ilo lachochedwa ndande yanu. Chitani chimwechi kwa kunikumbukila.”25Chimwechijha, pambuyo pakudya wadatenga chiko niwakamba, “Chikho ichi ni chipangano cha chipano cha Mnungu, chichimikizidwa kwa mwazi wanga. Chitani chimwechi kila yapo mkumwa, kwa kunikumbukila.”
26Pakuti kila yapo simujhidya bumunda ili ni kumwa mchikho ichi, muuzila wina Ambuye adafa ndande yanu mbaka yapo siwajhe.27Chimwecho, kila uyo wakudya bumunda la Ambuye, ni kumwa mchikho ichi ngati umo siifunikila, siwakhale wachita machimo kwa thupi ni mwazi wa Ambuye.28Ifunika, mundhu wajhipenyecheche mwene, ukali osadye bumunda ni kumwa mchikho.29Pakuti mundhu uyo wakudya ni kumwa, popande kujhiwa mate ya thupi la Ambuye, kwa kuchita chimwecho Mnungu siwakulange.30Nde ndande ambili pakati panu ali odwala ni ofooka, ni wina mbaka amwalila.31Nambho ngati tidakajipenyechecha bwino tikali osadye, Mnungu siwadaka tilamula.32Nambho yapo tilamulidwa ni kulangidwa ni Ambuye tijhikhala ni ulemu, ili sitidalangidwa pamojhi ni wandhu samkhulupilila Yesu.
33Chimwecho, abale wanga, yapo mkomanika kudya Chakudya cha Ambuye mjhilindana.34Mundhu wakakhala ni njala, wadye kukhomo lake, dala kukomanikana kwanu sikudakhala ndande ya kulamulidwa, ninghani ya yayo yakhalila sinikuyangheni yapo sinijhe kwanu.

The Word for the World International

https://app.library.bible/content/5f84a5b042979396