NEHEMIYA7nya_bib
1Khoma linamangidwa ndipo zitseko zinayikidwa. Pambuyo pake alonda a Nyumba ya Mulungu, oyimba nyimbo ndiponso Alevi anasankhidwa.2Kenaka ine ndinasankha mʼbale wanga Hanani pamodzi ndi Hananiya woyangʼanira nsanja yankhondo kukhala olamulira Yerusalemu chifukwa iyeyu anali munthu odalirika ndi woopa Mulungu kuposa anthu ena.3Ine ndinawawuza kuti, “Musalole kuti zipata za Yerusalemu zitsekulidwe mpaka dzuwa litatentha, ndipo alonda asanaweruke aonetsetse kuti atseka zitseko ndi kuzipiringidza. Musankhe alonda pakati pa anthu okhala mu Yerusalemu, ena akhale pa malo pawo ndi ena akhale moyangʼanana ndi nyumba zawo.”
Tsono chiwerengero cha anthu a ku Israeli chinali chotere:8Zidzukulu za Parosi2,1729Zidzukulu za Sefatiya37210Zidzukulu za Ara65211Zidzukulu za Pahati-Mowabu (kudzera mu mʼbado wa Yesuwa ndi Yowabu)2,81812Zidzukulu za Elamu1,25413Zidzukulu za Zatu84514Zidzukulu za Zakai76015Zidzukulu za Binuyi64816Zidzukulu za Bebai62817Zidzukulu za Azigadi2,32218Zidzukulu za Adonikamu66719Zidzukulu za Abigivai2,06720Zidzukulu za Adini65521Zidzukulu za Ateri (kudzera mwa Hezekiya)9822Zidzukulu za Hasumu32823Zidzukulu za Bezayi32424Zidzukulu za Harifu11225Zidzukulu za Gibiyoni95.26Anthu a ku Betelehemu ndi Netofa18827Anthu a ku Anatoti12828Anthu a ku Beti-Azimaveti4229Anthu a ku Kiriati Yeyarimu Kefira ndi Beeroti74330Anthu a ku Rama ndi Geba62131Anthu a ku Mikimasi12232Anthu a ku Beteli ndi Ai12333Anthu a ku Nebo winayo5234Ana a Elamu wina1,25435Zidzukulu za Harimu32036Zidzukulu za Yeriko34537Zidzukulu za Lodi, Hadidi ndi Ono72138Zidzukulu za Senaya3,930.39Ansembe anali awa: A banja la Yedaya (ndiye kuti zidzukulu za Yesuwa)97340Zidzukulu za Imeri1,05241Zidzukulu za Pasi-Huri1,24742Zidzukulu za Harimu1,017.43Alevi anali awa: A banja la Yesuwa ndi Kadimieli, ndiye kuti zidzukulu za Hodaviya74.44Anthu oyimba: Zidzukulu za Asafu148.45Alonda a ku Nyumba ya Mulungu anali awa: Zidzukulu zaSalumu, Ateri, Talimoni, Hatita ndi Sobai138.46Anthu ogwira ntchito ku Nyumba ya Mulungu anali awa: Zidzukulu zaZiha, zidzukulu za Hasufa, zidzukulu za Tabaoti,47Zidzukulu Kerosi, zidzukulu za Siya, zidzukulu za Padoni48Zidzukulu za Lebana za Hagaba, ndi za Salimayi,49Zidzukulu za Hanani, zidzukulu za Gideli, zidzukulu za Gahari,50Zidzukulu za Reyaya, zidzukulu za Rezini, zidzukulu za Nehoda,51Zidzukulu za Gazamu, zidzukulu za Uza, zidzukulu za Paseya,52Zidzukulu za Besai, zidzukulu za Meunimu, zidzukulu za Nefusimu,53Zidzukulu za Bakibuku, zidzukulu za Hakufa, zidzukulu za Harihuri,54Zidzukulu za Baziliti, zidzukulu za Mehida, zidzukulu za Harisa,55Zidzukulu za Barikosi, zidzukulu za Sisera, zidzukulu za Tema56Zidzukulu za Neziya, ndi zidzukulu za Hatifa.57Zidzukulu za antchito a Solomoni: Zidzukulu zaSotai, zidzukulu za Sofereti, zidzukulu za Perida58zidzukulu za Yaala, zidzukulu za Darikoni, zidzukulu za Gideli,59zidzukulu za Sefatiya, zidzukulu za Hatiluzidzukulu za Pokereti-Hazebaimu ndi zidzukulu Amoni.60Anthu onse ogwira ntchito ku Nyumba ya Mulungu pamodzi ndi zidzukulu za antchito a Solomoni analipo392.61Ali munsiwa anachokera ku Teli-Mela, Teri-Harisa, Kerubi, Adoni, ndi Imeri, koma sanathe kunena mwa tchutchutchu kuti makolo awo kapena mafuko awo analidi Aisraeli kapena ayi.62Zidzukulu zaDelaya, zidzukulu za Tobiya ndi zidzukulu za Nekoda642.63Ndiponso ena pakati pa ansembe anali awa: zidzukulu za Hobiya, zidzukulu za Hakozi ndi zidzukulu za Barizilai (munthu amene anakwatira mwana wamkazi wa Barizilai wa ku Giliyadi ndipo amatchedwa dzina limenelo).64Iwowa anafufuzafufuza mayina awo mʼbuku la mibado ya mabanja awo ndipo sanapeze mayina awo kotero anachotsedwa pa unsembe nawerengedwa ngati odetsedwa pa chipembedzo.65Choncho bwanamkubwa anawawuza anthuwo kuti asamadye nawo chakudya china chilichonse choperekedwa kwa Mulungu mpaka patapezeka wansembe wodziwa kugwiritsa bwino ntchito ya Urimu ndi Tumimu.66Chiwerengero chonse cha anthuwa chinali 42,360.67Kuwonjezera pamenepa panali antchito awo aamuna ndi aakazi 7,337 ndiponso anthu aamuna ndi aakazi oyimba nyimbo okwanira 245.68Panali akavalo 736, abulu angʼonoangʼono 245.69Ngamira zawo zinalipo 435 ndipo abulu analipo 6,720.70Atsogoleri ena a mabanja anapereka mphatso zothandizira ntchito. Bwanamkubwa anapereka ku thumba losungira chuma, ndalama zagolide za makilogalamu asanu ndi atatu, mabeseni makumi asanu ndi zovala za ansembe 530.71Atsogoleri ena amabanja anapereka ku thumba losungira chuma ndalama zagolide zokwana makilogalamu 168, ndiponso ndalama za siliva zokwana makilogalamu 1,250.72Anthu ena onse otsala anapereka ndalama zagolide zokwana makilogalamu 168, ndalama za siliva zokwana makilogalamu 140, ndiponso zovala za ansembe 67.73Choncho ansembe, Alevi, alonda a Nyumba ya Mulungu, anthu oyimba nyimbo, ena mwa anthu wamba, ogwira ntchito ku Nyumba ya Mulungu pamodzi ndi Aisraeli ena onse ankakhala mʼmizinda yawo. Ezara Awerenga Malamulo Pofika mwezi wachisanu ndi chiwiri Aisraeli onse anali atakhazikika mʼmizinda yawo.
Mndandanda wa Anthu Oyamba Kubwera Kuchokera ku Ukapolo
4Tsono mzinda wa Yerusalemu unali wotambasuka ndiponso waukulu koma munali anthu ochepa ndipo nyumba zinali zisanamangidwe.5Ndipo Mulungu wanga anayika mu mtima mwanga maganizo oti ndisonkhanitse anthu olemekezeka, akuluakulu ndi anthu onse kuti alembetse mayina mwa mabanja awo. Ndinapeza buku limene munalembedwa mayina a mabanja a iwo amene anayamba kubwera kuchokera ku ukapolo. Izi ndi zimene ndinazipeza zitalembedwa mʼmenemo:6Awa ndi anthu a mʼchigawo cha Yuda amene anabwerera kuchokera ku ukapolo amene Nebukadinezara mfumu ya Babuloni anawatenga ukapolo. Iwo anabwerera ku Yerusalemu ndi ku Yuda, aliyense ku mzinda wa makolo ake.7Anabwera pamodzi ndi atsogoleri awa: Zerubabeli, Yesuwa, Nehemiya, Azariya, Raamiya, Nahamani, Mordekai, Bilisani, Misipereti, Bigivai, Nehumu ndi Baana.Tsono chiwerengero cha anthu a ku Israeli chinali chotere:8Zidzukulu za Parosi2,1729Zidzukulu za Sefatiya37210Zidzukulu za Ara65211Zidzukulu za Pahati-Mowabu (kudzera mu mʼbado wa Yesuwa ndi Yowabu)2,81812Zidzukulu za Elamu1,25413Zidzukulu za Zatu84514Zidzukulu za Zakai76015Zidzukulu za Binuyi64816Zidzukulu za Bebai62817Zidzukulu za Azigadi2,32218Zidzukulu za Adonikamu66719Zidzukulu za Abigivai2,06720Zidzukulu za Adini65521Zidzukulu za Ateri (kudzera mwa Hezekiya)9822Zidzukulu za Hasumu32823Zidzukulu za Bezayi32424Zidzukulu za Harifu11225Zidzukulu za Gibiyoni95.26Anthu a ku Betelehemu ndi Netofa18827Anthu a ku Anatoti12828Anthu a ku Beti-Azimaveti4229Anthu a ku Kiriati Yeyarimu Kefira ndi Beeroti74330Anthu a ku Rama ndi Geba62131Anthu a ku Mikimasi12232Anthu a ku Beteli ndi Ai12333Anthu a ku Nebo winayo5234Ana a Elamu wina1,25435Zidzukulu za Harimu32036Zidzukulu za Yeriko34537Zidzukulu za Lodi, Hadidi ndi Ono72138Zidzukulu za Senaya3,930.39Ansembe anali awa: A banja la Yedaya (ndiye kuti zidzukulu za Yesuwa)97340Zidzukulu za Imeri1,05241Zidzukulu za Pasi-Huri1,24742Zidzukulu za Harimu1,017.43Alevi anali awa: A banja la Yesuwa ndi Kadimieli, ndiye kuti zidzukulu za Hodaviya74.44Anthu oyimba: Zidzukulu za Asafu148.45Alonda a ku Nyumba ya Mulungu anali awa: Zidzukulu zaSalumu, Ateri, Talimoni, Hatita ndi Sobai138.46Anthu ogwira ntchito ku Nyumba ya Mulungu anali awa: Zidzukulu zaZiha, zidzukulu za Hasufa, zidzukulu za Tabaoti,47Zidzukulu Kerosi, zidzukulu za Siya, zidzukulu za Padoni48Zidzukulu za Lebana za Hagaba, ndi za Salimayi,49Zidzukulu za Hanani, zidzukulu za Gideli, zidzukulu za Gahari,50Zidzukulu za Reyaya, zidzukulu za Rezini, zidzukulu za Nehoda,51Zidzukulu za Gazamu, zidzukulu za Uza, zidzukulu za Paseya,52Zidzukulu za Besai, zidzukulu za Meunimu, zidzukulu za Nefusimu,53Zidzukulu za Bakibuku, zidzukulu za Hakufa, zidzukulu za Harihuri,54Zidzukulu za Baziliti, zidzukulu za Mehida, zidzukulu za Harisa,55Zidzukulu za Barikosi, zidzukulu za Sisera, zidzukulu za Tema56Zidzukulu za Neziya, ndi zidzukulu za Hatifa.57Zidzukulu za antchito a Solomoni: Zidzukulu zaSotai, zidzukulu za Sofereti, zidzukulu za Perida58zidzukulu za Yaala, zidzukulu za Darikoni, zidzukulu za Gideli,59zidzukulu za Sefatiya, zidzukulu za Hatiluzidzukulu za Pokereti-Hazebaimu ndi zidzukulu Amoni.60Anthu onse ogwira ntchito ku Nyumba ya Mulungu pamodzi ndi zidzukulu za antchito a Solomoni analipo392.61Ali munsiwa anachokera ku Teli-Mela, Teri-Harisa, Kerubi, Adoni, ndi Imeri, koma sanathe kunena mwa tchutchutchu kuti makolo awo kapena mafuko awo analidi Aisraeli kapena ayi.62Zidzukulu zaDelaya, zidzukulu za Tobiya ndi zidzukulu za Nekoda642.63Ndiponso ena pakati pa ansembe anali awa: zidzukulu za Hobiya, zidzukulu za Hakozi ndi zidzukulu za Barizilai (munthu amene anakwatira mwana wamkazi wa Barizilai wa ku Giliyadi ndipo amatchedwa dzina limenelo).64Iwowa anafufuzafufuza mayina awo mʼbuku la mibado ya mabanja awo ndipo sanapeze mayina awo kotero anachotsedwa pa unsembe nawerengedwa ngati odetsedwa pa chipembedzo.65Choncho bwanamkubwa anawawuza anthuwo kuti asamadye nawo chakudya china chilichonse choperekedwa kwa Mulungu mpaka patapezeka wansembe wodziwa kugwiritsa bwino ntchito ya Urimu ndi Tumimu.66Chiwerengero chonse cha anthuwa chinali 42,360.67Kuwonjezera pamenepa panali antchito awo aamuna ndi aakazi 7,337 ndiponso anthu aamuna ndi aakazi oyimba nyimbo okwanira 245.68Panali akavalo 736, abulu angʼonoangʼono 245.69Ngamira zawo zinalipo 435 ndipo abulu analipo 6,720.70Atsogoleri ena a mabanja anapereka mphatso zothandizira ntchito. Bwanamkubwa anapereka ku thumba losungira chuma, ndalama zagolide za makilogalamu asanu ndi atatu, mabeseni makumi asanu ndi zovala za ansembe 530.71Atsogoleri ena amabanja anapereka ku thumba losungira chuma ndalama zagolide zokwana makilogalamu 168, ndiponso ndalama za siliva zokwana makilogalamu 1,250.72Anthu ena onse otsala anapereka ndalama zagolide zokwana makilogalamu 168, ndalama za siliva zokwana makilogalamu 140, ndiponso zovala za ansembe 67.73Choncho ansembe, Alevi, alonda a Nyumba ya Mulungu, anthu oyimba nyimbo, ena mwa anthu wamba, ogwira ntchito ku Nyumba ya Mulungu pamodzi ndi Aisraeli ena onse ankakhala mʼmizinda yawo. Ezara Awerenga Malamulo Pofika mwezi wachisanu ndi chiwiri Aisraeli onse anali atakhazikika mʼmizinda yawo.